Quran with Chichewa translation - Surah Al-haqqah ayat 14 - الحَاقة - Page - Juz 29
﴿وَحُمِلَتِ ٱلۡأَرۡضُ وَٱلۡجِبَالُ فَدُكَّتَا دَكَّةٗ وَٰحِدَةٗ ﴾
[الحَاقة: 14]
﴿وحملت الأرض والجبال فدكتا دكة واحدة﴾ [الحَاقة: 14]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo nthaka ndi mapiri nkuchotsedwa m’malo mwake ndi kuphwanyidwa kamodzi nkamodzi |