×

Ndipo pamene iwo achita chinthu chochititsa manyazi amati: “Tinapeza makolo athu ali 7:28 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:28) ayat 28 in Chichewa

7:28 Surah Al-A‘raf ayat 28 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 28 - الأعرَاف - Page - Juz 8

﴿وَإِذَا فَعَلُواْ فَٰحِشَةٗ قَالُواْ وَجَدۡنَا عَلَيۡهَآ ءَابَآءَنَا وَٱللَّهُ أَمَرَنَا بِهَاۗ قُلۡ إِنَّ ٱللَّهَ لَا يَأۡمُرُ بِٱلۡفَحۡشَآءِۖ أَتَقُولُونَ عَلَى ٱللَّهِ مَا لَا تَعۡلَمُونَ ﴾
[الأعرَاف: 28]

Ndipo pamene iwo achita chinthu chochititsa manyazi amati: “Tinapeza makolo athu ali kuchita ndipo Mulungu watilamula ife kutero.” Nena: “Iyayi; Mulungu salamula chinthu chimene chili chonyansa. Kodi inu muli kunena za Mulungu zimene simuzidziwa?”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإذا فعلوا فاحشة قالوا وجدنا عليها آباءنا والله أمرنا بها قل إن, باللغة نيانجا

﴿وإذا فعلوا فاحشة قالوا وجدنا عليها آباءنا والله أمرنا بها قل إن﴾ [الأعرَاف: 28]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo (osakhulupirira) akachita chauve amanena: “(Ichi) tidawapeza nacho makolo athu (akuchichita), ndiponso Allah watilamula chimenechi.” Nena: “Ndithu Allah salamula zonyansa. Kodi mukumunenera Allah zomwe simukuzidziwa?”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek