×

“Ndipo, ndithudi, iwo asocheza anthu ambiri. Ndipo Inu musaonjeze china chili chonse 71:24 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Nuh ⮕ (71:24) ayat 24 in Chichewa

71:24 Surah Nuh ayat 24 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Nuh ayat 24 - نُوح - Page - Juz 29

﴿وَقَدۡ أَضَلُّواْ كَثِيرٗاۖ وَلَا تَزِدِ ٱلظَّٰلِمِينَ إِلَّا ضَلَٰلٗا ﴾
[نُوح: 24]

“Ndipo, ndithudi, iwo asocheza anthu ambiri. Ndipo Inu musaonjeze china chili chonse kwa anthu ochita zoipa chifukwa apitirizabe kuchita zoipa.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وقد أضلوا كثيرا ولا تزد الظالمين إلا ضلالا, باللغة نيانجا

﴿وقد أضلوا كثيرا ولا تزد الظالمين إلا ضلالا﴾ [نُوح: 24]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo ndithu iwo asokeretsa (anthu) ambiri; ndipo musawaonjezere ochita zoipa (china chake) koma kusokera basi.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek