Quran with Chichewa translation - Surah Al-Jinn ayat 20 - الجِن - Page - Juz 29
﴿قُلۡ إِنَّمَآ أَدۡعُواْ رَبِّي وَلَآ أُشۡرِكُ بِهِۦٓ أَحَدٗا ﴾ 
[الجِن: 20]
﴿قل إنما أدعو ربي ولا أشرك به أحدا﴾ [الجِن: 20]
| Khaled Ibrahim Betala “Nena: “Ndikumpembedza Mbuye wanga M’modzi (Yekha) ndipo sindingamphatikize ndi aliyense (m’mapemphero Ake).” |