Quran with Chichewa translation - Surah Al-Jinn ayat 19 - الجِن - Page - Juz 29
﴿وَأَنَّهُۥ لَمَّا قَامَ عَبۡدُ ٱللَّهِ يَدۡعُوهُ كَادُواْ يَكُونُونَ عَلَيۡهِ لِبَدٗا ﴾
[الجِن: 19]
﴿وأنه لما قام عبد الله يدعوه كادوا يكونون عليه لبدا﴾ [الجِن: 19]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo ndithu pamene adaima kapolo wa Allah (Muhammad{s.a.w}, pa Swala yake) uku akumpembedza (Allah), ziwanda zidatsala pang’ono kumgwera (chifukwa cha kuchuluka kwawo ndi kumzinga podabwa ndi zimene adaziona ndi kuzimva) |