Quran with Chichewa translation - Surah Al-Muddaththir ayat 56 - المُدثر - Page - Juz 29
﴿وَمَا يَذۡكُرُونَ إِلَّآ أَن يَشَآءَ ٱللَّهُۚ هُوَ أَهۡلُ ٱلتَّقۡوَىٰ وَأَهۡلُ ٱلۡمَغۡفِرَةِ ﴾
[المُدثر: 56]
﴿وما يذكرون إلا أن يشاء الله هو أهل التقوى وأهل المغفرة﴾ [المُدثر: 56]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo sangakumbukire pokhapokha Allah atafuna. Iye ndiye Amene ali woyenera kumuopa, ndiponso ndiye Mwini kukhululukira (amene akumuopa) |