Quran with Chichewa translation - Surah ‘Abasa ayat 37 - عَبَسَ - Page - Juz 30
﴿لِكُلِّ ٱمۡرِيٕٖ مِّنۡهُمۡ يَوۡمَئِذٖ شَأۡنٞ يُغۡنِيهِ ﴾
[عَبَسَ: 37]
﴿لكل امرئ منهم يومئذ شأن يغنيه﴾ [عَبَسَ: 37]
Khaled Ibrahim Betala “Munthu aliyense mwa iwo, tsiku limenelo adzakhala ndi zakezake zotangwanika nazo. (Sadzalabadira za anzake) |