Quran with Chichewa translation - Surah Az-Zalzalah ayat 6 - الزَّلزَلة - Page - Juz 30
﴿يَوۡمَئِذٖ يَصۡدُرُ ٱلنَّاسُ أَشۡتَاتٗا لِّيُرَوۡاْ أَعۡمَٰلَهُمۡ ﴾
[الزَّلزَلة: 6]
﴿يومئذ يصدر الناس أشتاتا ليروا أعمالهم﴾ [الزَّلزَلة: 6]
Khaled Ibrahim Betala “Tsiku limenelo anthu adzachoka (m’manda) ali m’magulu obalalika kuti akasonyezedwe ntchito zawo (ndikudziwa chiwerengero chawo chimene chili kwa Allah) |