Quran with Chichewa translation - Surah Hud ayat 83 - هُود - Page - Juz 12
﴿مُّسَوَّمَةً عِندَ رَبِّكَۖ وَمَا هِيَ مِنَ ٱلظَّٰلِمِينَ بِبَعِيدٖ ﴾
[هُود: 83]
﴿مسومة عند ربك وما هي من الظالمين ببعيد﴾ [هُود: 83]
Khaled Ibrahim Betala “(Sangalawezo) zokhala ndi zizindikiro kwa Mbuye wako. (Sangalawe iliyonse idali ndi mwini wake); ndipo chilango chimenechi sichili kutali ndi anthu oipa |