Quran with Chichewa translation - Surah Al-Mulk ayat 1 - المُلك - Page - Juz 29
﴿تَبَٰرَكَ ٱلَّذِي بِيَدِهِ ٱلۡمُلۡكُ وَهُوَ عَلَىٰ كُلِّ شَيۡءٖ قَدِيرٌ ﴾
[المُلك: 1]
﴿تبارك الذي بيده الملك وهو على كل شيء قدير﴾ [المُلك: 1]
Khaled Ibrahim Betala “۞ Watukuka ndi kudalitsika (Allah) Amene m’manja Mwake muli ufumu (wochita chilichonse pazolengedwa zonse); ndipo Iye ali ndi mphamvu yokwanira pachilichonse |