Quran with Chichewa translation - Surah Al-haqqah ayat 11 - الحَاقة - Page - Juz 29
﴿إِنَّا لَمَّا طَغَا ٱلۡمَآءُ حَمَلۡنَٰكُمۡ فِي ٱلۡجَارِيَةِ ﴾
[الحَاقة: 11]
﴿إنا لما طغى الماء حملناكم في الجارية﴾ [الحَاقة: 11]
Khaled Ibrahim Betala “Ndithu pamene madzi adasefukira mopyola muyeso (mpaka kumeza mapiri nthawi ya chigumula cha Nowa) Ife tidakukwezani mchombo choyandama ndi kuyenda |