Quran with Chichewa translation - Surah Al-Muddaththir ayat 37 - المُدثر - Page - Juz 29
﴿لِمَن شَآءَ مِنكُمۡ أَن يَتَقَدَّمَ أَوۡ يَتَأَخَّرَ ﴾
[المُدثر: 37]
﴿لمن شاء منكم أن يتقدم أو يتأخر﴾ [المُدثر: 37]
Khaled Ibrahim Betala “Kwa yemwe wafuna mwa inu kutsogola (pochita zabwino zokamthandiza tsiku louka kwa akufa) kapena kutsalira (ndi za m’dziko) |