Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qiyamah ayat 13 - القِيَامة - Page - Juz 29
﴿يُنَبَّؤُاْ ٱلۡإِنسَٰنُ يَوۡمَئِذِۭ بِمَا قَدَّمَ وَأَخَّرَ ﴾
[القِيَامة: 13]
﴿ينبأ الإنسان يومئذ بما قدم وأخر﴾ [القِيَامة: 13]
Khaled Ibrahim Betala “Tsiku limenelo munthu adzauzidwa zochita zake zimene adazitsogoza ndi zimene adazichedwetsa |