Quran with Chichewa translation - Surah Al-Inshiqaq ayat 6 - الانشِقَاق - Page - Juz 30
﴿يَٰٓأَيُّهَا ٱلۡإِنسَٰنُ إِنَّكَ كَادِحٌ إِلَىٰ رَبِّكَ كَدۡحٗا فَمُلَٰقِيهِ ﴾
[الانشِقَاق: 6]
﴿ياأيها الإنسان إنك كادح إلى ربك كدحا فملاقيه﴾ [الانشِقَاق: 6]
Khaled Ibrahim Betala “E iwe munthu! Ndithudi iwe ukubwerera kwa Mbuye wako (ndi zochita zako zabwino kapena zoipa), kubwerera kotsimikizika, ndipo iwe ukumana (ndi zotsatira za zochitachita zako) |