القرآن باللغة نيانجا - سورة الضحى مترجمة إلى اللغة نيانجا، Surah Duha in Chichewa. نوفر ترجمة دقيقة سورة الضحى باللغة نيانجا - Chichewa, الآيات 11 - رقم السورة 93 - الصفحة 596.
وَالضُّحَىٰ (1) Pali usana |
وَاللَّيْلِ إِذَا سَجَىٰ (2) Ndi pali usiku pamene ulipo |
مَا وَدَّعَكَ رَبُّكَ وَمَا قَلَىٰ (3) Ambuye wako sadakutaye iwe ndiponso sakudana nawe ayi |
وَلَلْآخِرَةُ خَيْرٌ لَّكَ مِنَ الْأُولَىٰ (4) Ndipo, ndithudi, moyo umene uli nkudza ndi wabwino kwa iwe kuposa moyo uno |
وَلَسَوْفَ يُعْطِيكَ رَبُّكَ فَتَرْضَىٰ (5) Ndithudi Ambuye wako adzakupatsa, ndipo iwe chidzakukondweretsa |
أَلَمْ يَجِدْكَ يَتِيمًا فَآوَىٰ (6) Kodi sadakupeze iwe uli wa masiye ndipo adakupatsa malo okhala |
وَوَجَدَكَ ضَالًّا فَهَدَىٰ (7) Kodi sadakupeze uli wosochera ndipo Iye adakutsogolera |
وَوَجَدَكَ عَائِلًا فَأَغْنَىٰ (8) Kodi sadakupeze iwe waumphawi ndipo adakulemeretsa |
فَأَمَّا الْيَتِيمَ فَلَا تَقْهَرْ (9) Motero iwe usapondereze pansi mwana wa masiye |
وَأَمَّا السَّائِلَ فَلَا تَنْهَرْ (10) Ndipo usapirikitse munthu wopempha |
وَأَمَّا بِنِعْمَةِ رَبِّكَ فَحَدِّثْ (11) Koma lengeza chisomo cha a Ambuye wako |